Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 4:9 - Buku Lopatulika

9 Benedekere ku Makazi ndi Saalibimu ndi Betesemesi ndi Elonibetehanani;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Benedekere ku Makazi ndi Saalibimu ndi Betesemesi ndi Elonibetehanani;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Benedekere ku mizinda iyi: Makazi, Salabimu, Betesemesi, Etoni ndi Betehanani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Beni-Dekeri, woyangʼanira mizinda ya Makazi, Saalibimu, Beti-Semesi ndi Eloni Beti-Hanani;

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 4:9
8 Mawu Ofanana  

Ndipo malire anazungulira kuyambira ku Baala kunka kumadzulo, kuphiri la Seiri, napitirira kumbali kwa phiri la Yearimu kumpoto, ndilo Kesaloni, natsikira ku Betesemesi, napitirira ku Timna;


Saalabini, ndi Ayaloni ndi Itila;


ndi Eloni ndi Timna ndi Ekeroni;


ndi Aini ndi mabusa ake, ndi Yuta ndi mabusa ake, ndi Betesemesi ndi mabusa ake; mizinda isanu ndi inai yotapira mafuko awiri aja.


Aamori anakhumbanso kukhala kuphiri la Heresi, ku Ayaloni, ndi ku Saalibimu; koma dzanja la a m'nyumba ya Yosefe linawagonjetsa, nakhala iwo akupereka msonkho.


Ndipo ng'ombezo zinatsata njira yolunjika ku Betesemesi, zinali kuyenda mumseu, zilikulira; sizinapatukire ku dzanja lamanja, kapena kulamanzere; ndipo mafumu a Afilisti anazitsatira kufikira ku malire a Betesemesi.


Ndipo a ku Betesemesi anati, Akhoza ndani kuima pamaso pa Yehova, Mulungu Woyera uyu? Ndipo adzakwera kwa yani pakutichokera ife?


Ndipo muyang'anire, ngati likwera panjira ya malire akeake ku Betesemesi, Iye anatichitira choipa ichi chachikulu; koma likapanda kutero, tidzadziwapo kuti dzanja limene linatikantha, silili lake; langotigwera tsokali.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa