1 Mafumu 4:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo maina ao ndiwo: Benihuri anatengetsa ku mapiri a Efuremu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo maina ao ndiwo: Benihuri anatengetsa ku mapiri a Efuremu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Maina ndi aŵa: Benihuri, ku dziko lamapiri la Efuremu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mayina awo ndi awa: Beni-Huri, wa ku dziko la mapiri la Efereimu; Onani mutuwo |