1 Mafumu 4:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Solomoni anali nao akapitao khumi ndi awiri akuyang'anira Aisraele onse, akufikitsira mfumu ndi banja lake zakudya; aliyense anafikitsa zakudya zofikira mwezi umodzi wa chaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Solomoni anali nao akapitao khumi ndi awiri akuyang'anira Aisraele onse, akufikitsira mfumu ndi banja lake zakudya; aliyense anafikitsa zakudya zofikira mwezi umodzi wa chaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Solomoni anali ndi nduna khumi ndi ziŵiri zimene adaziika m'zigawo zonse za dziko la Israele. Nduna zimenezi zinkapereka chakudya kwa mfumu ndi banja lake lonse. Nduna iliyonse inkapereka chakudya mwezi umodzi pa chaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Solomoni analinso ndi abwanamkubwa khumi ndi awiri amene ankayangʼanira zigawo zonse za dziko la Israeli. Iwo ankapereka chakudya kwa mfumu ndiponso ku banja laufumu. Bwanamkubwa aliyense ankapereka chakudya mwezi umodzi pa chaka. Onani mutuwo |