1 Mafumu 4:4 - Buku Lopatulika4 ndi Benaya mwana wa Yehoyada anali kazembe wa nkhondo, ndi Zadoki ndi Abiyatara anali ansembe, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi Benaya mwana wa Yehoyada anali kazembe wa nkhondo, ndi Zadoki ndi Abiyatara anali ansembe, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Benaya mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wankhondo. Zadoki ndi Abiyatara anali ansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Benaya mwana wa Yehoyada, anali mtsogoleri wa ankhondo; Zadoki ndi Abiatara, anali ansembe; Onani mutuwo |