1 Mafumu 4:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo akapitao aja anatengetsera chakudya Solomoni ndi anthu onse akudya ku gome la mfumu Solomoni, munthu yense m'mwezi mwake, sanalole kanthu kasoweke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo akapitao aja anatengetsera chakudya Solomoni ndi anthu onse akudya ku gome la mfumu Solomoni, munthu yense m'mwezi mwake, sanalole kanthu kasoweke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Tsono nduna khumi ndi ziŵiri zija zinkapereka chakudya cha mfumu Solomoni ndi cha anthu onse amene ankadzadya nao kunyumba kwa mfumu, nduna iliyonse mwezi wake. Ndunazo sizinkalola kuti kanthu kalikonse kasoŵe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Abwanamkubwa a zigawo aja, aliyense pa mwezi wake, ankapereka chakudya cha Mfumu Solomoni ndi cha anthu onse amene ankadya naye. Iwo ankaonetsetsa kuti pasasowe kalikonse. Onani mutuwo |
Ndipo ana a Israele monga mwa chiwerengo chao, kunena za akulu a nyumba za makolo ao, ndi akazembe a zikwi, ndi a mazana, ndi akapitao ao akutumikira mfumu mu ntchito iliyonse ya magawidwe, akulowa ndi kutuluka mwezi ndi mwezi, miyezi yonse ya chaka, chigawo chilichonse ncha amuna zikwi makumi awiri mphambu zinai.