Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 4:26 - Buku Lopatulika

26 Ndipo Solomoni anali nazo zipinda za akavalo a magaleta ake zikwi khumi mphambu ziwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Ndipo Solomoni anali nazo zipinda za akavalo a magaleta ake zikwi khumi mphambu ziwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Ndipo Solomoni anali ndi zipinda 40,000 zosungiramo akavalo okoka magareta ake, analinso ndi anthu 12,000 okwera pa akavalo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Solomoni anali ndi zipinda 4,000 zodyeramo akavalo okoka magaleta ake ndi anthu 12,000 oyendetsa magaleta.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 4:26
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anatenga apakavalo ake chikwi chimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri, ndi oyenda pansi zikwi makumi awiri; ndipo Davide anadula mitsita akavalo onse a magaleta, koma anasunga a iwo akufikira magaleta zana limodzi.


Ndipo akapitao aja anatengetsera chakudya Solomoni ndi anthu onse akudya ku gome la mfumu Solomoni, munthu yense m'mwezi mwake, sanalole kanthu kasoweke.


ndi mizinda yonse yosungamo zinthu zake za Solomoni, ndi mizinda yosungamo magaleta ake, ndi mizinda yokhalamo apakavalo ake, ndi zina zilizonse zidakomera Solomoni kuzimanga mu Yerusalemu, ndi ku Lebanoni, ndi m'dziko lonse la ufumu wake.


Ndipo Solomoni anasonkhanitsa magaleta ndi apakavalo, nakhala nao magaleta chikwi chimodzi mphambu mazana anai, ndi apakavalo zikwi khumi ndi ziwiri; nawaika m'mizinda ya magaleta ndi kwa mfumu ku Yerusalemu.


Ndipo Solomoni anali nazo zipinda zikwi zinai za akavalo ndi magaleta, ndi apakavalo zikwi khumi ndi ziwiri; nawaika m'mizinda ya magaleta, ndi mu Yerusalemu kwa mfumu.


Ena atama magaleta, ndi ena akavalo; koma ife tidzatchula dzina la Yehova Mulungu wathu.


Koma asadzichulukitsire akavalo iye, kapena kubwereretsa anthu anke ku Ejipito, kuti achulukitse akavalo; popeza Yehova anati nanu, Musamabwereranso njira iyi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa