1 Mafumu 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo akulu a mfumu ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo akulu a mfumu ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 ndipo nduna zake zikuluzikulu zinali izi: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Nduna zake zikuluzikulu zinali izi: Azariya mwana wa Zadoki anali wansembe; Onani mutuwo |