1 Mafumu 4:19 - Buku Lopatulika19 Gebere mwana wa Uri ku dziko la Giliyadi, dziko la Sihoni mfumu ya Aamori, ndi la Ogi mfumu ya Basani; munalibe kapitao wina m'deramo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Gebere mwana wa Uri ku dziko la Giliyadi, dziko la Sihoni mfumu ya Aamori, ndi la Ogi mfumu ya Basani; munalibe kapitao wina m'deramo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Gebere, mwana wa Uri, ankayang'anira ku dziko la Giliyadi kuphatikizapo dziko limene lidaali la Sihoni mfumu ya Aamori, ndiponso la Ogi mfumu ya ku Basani. Panalinso nduna yaikulu imodzi yoyang'anira dziko lonse la Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Geberi mwana wa Uri, anali woyangʼanira Giliyadi (dziko la Sihoni mfumu ya Aamori ndi dziko la Ogi mfumu ya Basani). Iye ankayangʼanira chigawo chonsechi yekha. Onani mutuwo |