1 Mafumu 4:10 - Buku Lopatulika10 Benihesedi ku Aruboti ndi Soko ndi dziko lonse la Hefere; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Benihesedi ku Aruboti ndi Soko ndi dziko lonse la Hefere; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Benihesedi ankayang'anira ku mzinda wa Aruboti. Ankayang'aniranso Soko ndi dziko lonse la Hefere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Beni-Hesedi, woyangʼanira mizinda ya Aruboti (Soko ndi dziko lonse la Heferi); Onani mutuwo |