Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 20:3 - Buku Lopatulika

3 Atero Benihadadi, Siliva wako ndi golide wako ndi wanga, akazi ako ndi ana ako omwe okometsetsawo ndi anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Atero Benihadadi, Siliva wako ndi golide wako ndi wanga, akazi ako ndi ana ako omwe okometsetsawo ndi anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 awapatse amithengawo siliva wake pamodzi ndi golide yemwe. Akazi ake okongola, pamodzi ndi ana omwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 “Beni-Hadadi akuti, ‘Siliva wako ndi golide wako ndi wanga, ndipo akazi ako okongola ndi ana ako ndi anganso.’ ”

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 20:3
5 Mawu Ofanana  

Natumiza mithenga kumzinda kwa Ahabu mfumu ya Israele, nati kwa iye,


Motero anavala chiguduli m'chuuno mwao, ndi zingwe pamitu pao, nafika kwa mfumu ya Israele, nati, Kapolo wanu Benihadadi ati, Ndiloleni ndikhale ndi moyo. Nati iye, Akali moyo kodi? Ndiye mbale wanga.


Ndipo mfumu ya Israele anayankha, nati, Monga mwanena, mbuye wanga mfumu, ndine wanu ndi zonse ndili nazo.


Mdani anati, Ndiwalondola, ndiwapeza, ndidzagawa zofunkha; ndidzakhuta nao mtima; ndidzasolola lupanga langa, dzanja langa lidzawaononga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa