Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 2:41 - Buku Lopatulika

41 Ndipo anamuuza Solomoni, kuti, Simei wachoka ku Yerusalemu kunka ku Gati, nabweranso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Ndipo anamuuza Solomoni, kuti, Simei wachoka ku Yerusalemu kunka ku Gati, nabweranso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Tsono Solomoni atamva kuti Simei adaapita ku Gati kuchoka ku Yerusalemu, ndipo kuti adabwerako,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Solomoni atawuzidwa kuti Simei anatuluka mu Yerusalemu ndi kupita ku Gati ndipo kuti wabwerako,

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 2:41
2 Mawu Ofanana  

Ndipo Simei ananyamuka, namangirira mbereko pabulu wake, nanka ku Gati kwa Akisi kukafuna akapolo ake; namuka Simei, nabwera nao akapolo ake kuchokera ku Gati.


Ndipo mfumu inatuma munthu kukaitana Simei, niti kwa iye, Kodi sindinakulumbiritse pa Yehova ndi kukuchenjeza, kuti, Tadziwa ndithu, kuti tsiku lakutuluka iwe ndi kukayenda kwina konse udzafa ndithu? Ndipo iwe unati kwa ine, Mau amene ndawamva ndi abwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa