1 Mafumu 2:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo iye anati, Abisagi wa ku Sunamu apatsidwe kwa Adoniya mbale wanu akhale mkazi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo iye anati, Abisagi wa ku Sunamu apatsidwe kwa Adoniya mbale wanu akhale mkazi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Maiyo adati, “Mulole kuti Abisagi Msunamu uja apatsidwe kwa Adoniya mbale wanu, kuti akhale mkazi wake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndipo amayiwo anati, “Mulole kuti Abisagi wa ku Sunemu akhale mkazi wa mʼbale wanu Adoniya.” Onani mutuwo |