1 Mafumu 2:20 - Buku Lopatulika20 Pamenepo mkaziyo anati, Ndikupemphani kapempho kamodzi, musandikaniza. Ndipo mfumu inati kwa iye, Tapemphani amai wanga, popeza sindikukanizani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pamenepo mkaziyo anati, Ndikupemphani kapempho kamodzi, musandikaniza. Ndipo mfumu inati kwa iye, Tapemphani amai wanga, popeza sindikukanizani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ndipo maiyo adati, “Ndikufuna kukupemphani kanthu kakang'ono. Chonde musandikanize.” Tsono mfumu idauza mai wakeyo kuti, “Pemphani chimene mukufuna, mai wanga, sindikukanizani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Amayi akewo anati, “Ndikufuna ndikupempheni kanthu kakangʼono. Chonde musandikanize.” Mfumu inayankha kuti, “Pemphani amayi, ine sindikukanizani.” Onani mutuwo |