1 Mafumu 2:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Bateseba anati, Chabwino, ndidzakunenera kwa mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Bateseba anati, Chabwino, ndidzakunenera kwa mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Bateseba adati, “Chabwino. Ndikulankhulira kwa mfumu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Batiseba anayankha kuti, “Chabwino. Ndidzakuyankhulira kwa mfumu.” Onani mutuwo |