Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 2:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo tsopano, ndikupemphani pempho limodzi, musandikaniza. Ndipo mkaziyo anati kwa iye, Tanena.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo tsopano, ndikupemphani pempho limodzi, musandikaniza. Ndipo mkaziyo anati kwa iye, Tanena.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Tsopano ndikukupemphani chinthu chimodzi. Musandikanize ai.” Bateseba adati, “Nena.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Tsono ndili ndi pempho limodzi kwa inu. Musandikanize ayi.” Batiseba anati, “Nena.”

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 2:16
5 Mawu Ofanana  

Nati iye, Mudziwa kuti ufumu unali wanga, ndi kuti Aisraele onse anaika maso ao pa ine, kuti ndikhale mfumu ndine; koma ufumu watembenuka nukhala wa mbale wanga, popeza iye anaulandira kwa Yehova.


Nati iye, Mundinenere kwa mfumu Solomoni, popeza sakukanizani, kuti andipatse Abisagi wa ku Sunamu akhale mkazi wanga.


Pamenepo mkaziyo anati, Ndikupemphani kapempho kamodzi, musandikaniza. Ndipo mfumu inati kwa iye, Tapemphani amai wanga, popeza sindikukanizani.


Chifukwa cha Davide mtumiki wanu musabweze nkhope ya wodzozedwa wanu.


Zinthu ziwiri ndakupemphani, musandimane izo ndisanamwalire:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa