Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 17:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo kudzakhala kuti uzikamwa mumtsinje, ndipo ndalamulira makwangwala kukudyetsa kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo kudzakhala kuti uzikamwa mumtsinje, ndipo ndalamulira makungubwi kukudyetsa kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Uzikamwa mumtsinjemo, ndipo ndalamula makwangwala kuti azikakudyetsa kumeneko.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Uzikamwa mu mtsinjemo, ndipo ndalamula makwangwala kuti azikakudyetsa kumeneko.”

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 17:4
15 Mawu Ofanana  

Namuka iye, napeza mtembo wake wogwera m'njira, ndi bulu ndi mkango zili chiimire pafupi ndi mtembo. Mkango udalibe kudya mtembo, kapena kukadzula bulu.


Choka kuno, nutembenukire kum'mawa, ukabisale kumtsinje Keriti uli ku Yordani.


Momwemo iye anamuka, nachita monga mwa mau a Yehova, nakakhala kumtsinje Keriti uli ku Yordani.


Nyamuka, pita ku Zarefati wa ku Sidoni, nukhale kumeneko; taona, ndamlamulira mkazi wamasiye wa kumeneko akudyetse.


Iye akapatsa mpumulo adzamtsutsa ndani? Akabisa nkhope yake adzampenyerera ndani? Chikachitika pa mtundu wa anthu, kapena pa munthu, nchimodzimodzi;


Amkonzeratu khwangwala chakudya chake ndani, pamenepo ana ake afuulira kwa Mulungu, naulukauluka osowa chakudya?


Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Pamenepo Yona anapemphera kwa Yehova Mulungu wake ali m'mimba mwa nsombayo.


Tenga ndodoyo, nusonkhanitse khamulo; iwe ndi Aroni mbale wako, munene ndi thanthwe pamaso pao, kuti liwapatse madzi; potero uwatulutsire madzi m'thanthwe, ndi kumwetsa khamu la anthu ndi zoweta zao.


Pomwepo mdierekezi anamsiya Iye, ndipo onani, angelo anadza, namtumikira Iye.


Koma Iye anayankha nati, Kwalembedwa, Munthu sadzakhala ndi moyo ndi mkate wokha, koma ndi mau onse akutuluka m'kamwa mwa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa