Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 17:3 - Buku Lopatulika

3 Choka kuno, nutembenukire kum'mawa, ukabisale kumtsinje Keriti uli ku Yordani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Choka kuno, nutembenukire kum'mawa, ukabisale kumtsinje Keriti uli ku Yordani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 “Chokako kuno, upite chakuvuma, ukabisale ku mtsinje wa Keriti, kuvuma kwa Yordani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 “Choka kuno, upite kummawa, ukabisale mʼmbali mwa mtsinje wa Keriti, pafupi ndi Yorodani.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 17:3
12 Mawu Ofanana  

Ndipo mau a Yehova anadza kwa iye, nati,


Ndipo kudzakhala kuti uzikamwa mumtsinje, ndipo ndalamulira makwangwala kukudyetsa kumeneko.


Mikaya nati, Taona, udzapenya tsiku lolowa iwe m'chipinda cha pakati kubisala.


Pobisalira pamaso panu mudzawabisa kwa chiwembu cha munthu, mudzawabisa iwo mumsasa kuti muwalanditse pa kutetana kwa malilime.


Apangana mochenjerera pa anthu anu, nakhalira upo pa obisika anu.


Ndipo akulu anati kwa Baruki, Pita, nubisale iwe ndi Yeremiya; munthu yense asadziwe kumene muli.


Ndipo mfumu inauza Yerameele mwana wake wa mfumu, ndi Seraya mwana wa Aziriele, ndi Selemiya mwana wa Abideele, kuti awagwire Baruki mlembi ndi Yeremiya mneneri; koma Yehova anawabisa.


Pamenepo anatola miyala kuti amponye Iye; koma Yesu anabisala, natuluka mu Kachisi.


Pomwepo abale anatulutsa Paulo amuke kufikira kunyanja; koma Silasi ndi Timoteo anakhalabe komweko.


(amenewo dziko lapansi silinayenere iwo), osokerera m'mapululu, ndi m'mapiri, ndi m'mapanga, ndi m'mauna a dziko.


Ndipo anapatsa mkazi mapiko awiri a chiombankhanga chachikulu, kuti akaulukire kuchipululu, ku mbuto yake, kumene adyetsedwako nthawi, ndi zinthawi, ndi nusu la nthawi, osapenya nkhope ya njoka.


Ndipo mkazi anathawira kuchipululu, kumene ali nayo mbuto yokonzekeratu ndi Mulungu, kuti kumeneko akamdyetse masiku chikwi chimodzi ndi mazana awiri mphambu makumi asanu ndi limodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa