1 Mafumu 16:6 - Buku Lopatulika6 Nagona Baasa ndi makolo ake, naikidwa ku Tiriza; ndipo Ela mwana wake analowa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Nagona Baasa ndi makolo ake, naikidwa ku Tiriza; ndipo Ela mwana wake analowa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Baasa adamwalira, naikidwa m'manda ku Tiriza. Ndipo Ela mwana wake ndiye adaloŵa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Baasa anamwalira nayikidwa mʼmanda amene anayikidwa makolo ake ku Tiriza. Ndipo Ela mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake. Onani mutuwo |