Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 16:5 - Buku Lopatulika

5 Tsono machitidwe ena a Baasa, ndi ntchito zake, ndi mphamvu zake, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Tsono machitidwe ena a Baasa, ndi ntchito zake, ndi mphamvu zake, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ntchito zina za Baasa ndi zonse zamphamvu zimene adachita, zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Tsono ntchito zina za Baasa ndi zamphamvu zake zimene anachita, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Israeli?

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 16:5
5 Mawu Ofanana  

Ndipo machitidwe ena a Yerobowamu m'mene umo anachitira ufumu, taona, analembedwa m'buku la machitidwe a mafumu a Israele.


Ndipo machitidwe ena a Nadabu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Tsono machitidwe ena a Ela, ndi ntchito zake zonse, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Machitidwe ena tsono a Zimiri, ndi chiwembu anachichitacho, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Israele?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa