1 Mafumu 16:4 - Buku Lopatulika4 Agalu adzadya aliyense wa Baasa amene adzafera m'mzinda, ndipo amene adzafera m'thengo zidzamudya mbalame za m'mlengalenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Agalu adzadya aliyense wa Baasa amene adzafera m'mudzi, ndipo amene adzafera m'thengo zidzamudya mbalame za m'mlengalenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Aliyense wa banja la Baasa amene adzafere mu mzinda, agalu adzamudya. Ndipo aliyense amene adzafere ku thengo, mbalame zamumlengalenga zidzamudya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Agalu adzadya aliyense wa banja la Baasa amene adzafere mu mzinda, ndipo mbalame za mu mlengalenga zidzadya iwo amene adzafere kuthengo.” Onani mutuwo |