Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 16:3 - Buku Lopatulika

3 taona, ndidzachotsa psiti Baasa ndi nyumba yake, ndipo ndidzafanizitsa nyumba yako ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 taona, ndidzachotsa psiti Baasa ndi nyumba yake, ndipo ndidzafanizitsa nyumba yako ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ndithudi ndidzakufafaniza kotheratu pamodzi ndi banja lako lonse, monga m'mene ndidachitira banja la Yerobowamu mwana wa Nebati.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Taonani, Ine ndatsala pangʼono kuwononga Baasa pamodzi ndi nyumba yake, ndipo ndidzachitira nyumba yake zimene ndinachita pa nyumba ya Yeroboamu mwana wa Nebati.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 16:3
8 Mawu Ofanana  

chifukwa chake, taona ndidzafikitsa choipa pa nyumba ya Yerobowamu, ndi kugulula mwana wamwamuna yense wa Yerobowamu womangika ndi womasuka mu Israele, ndipo ndidzachotsa psiti nyumba yonse ya Yerobowamu, monga munthu achotsa ndowe kufikira idatha yonse.


Agalu adzadya aliyense wa Yerobowamu wakufa m'mzinda; ndi mbalame za m'mlengalenga zidzadya yense wakufera kuthengo; popeza wanena ndi Yehova.


Ndipo ndidzalinganiza nyumba ya Ahabu ndi nyumba ya Yerobowamu mwana wa Nebati, ndi nyumba ya Baasa mwana wa Ahiya.


Ndipo iwo adzatuluka ndi kuyang'ana mitembo ya anthu amene andilakwira Ine, pakuti mphutsi yao sidzafa, pena moto wao sudzazimidwa; ndipo iwo adzanyansa anthu onse.


Adzamuika monga kuika bulu, adzamkoka nadzamponya kunja kwa zipata za Yerusalemu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa