1 Mafumu 15:8 - Buku Lopatulika8 Nagona Abiya ndi makolo ake, namuika anthu m'mzinda wa Davide; Asa mwana wake nalowa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Nagona Abiya ndi makolo ake, namuika anthu m'mudzi wa Davide; Asa mwana wake nalowa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Abiya adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo mu mzinda wa Davide. Ndipo Asa mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndipo Abiya anamwalira nayikidwa mʼmanda momwe anayikidwa makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndipo Asa, mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake. Onani mutuwo |