Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 15:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobowamu masiku onse a moyo wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobowamu masiku onse a moyo wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobowamu masiku onse a moyo wa Abiyayo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Panali nkhondo pakati pa Rehobowamu ndi Yeroboamu masiku onse a moyo wa Abiya.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 15:6
3 Mawu Ofanana  

Tsono, machitidwe ake ena a Rehobowamu, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?


Ndipo panali nkhondo pakati pa Rehobowamu ndi Yerobowamu masiku ao onse.


Ndipo machitidwe ake ena a Abiya, ndi zonse anazichita, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda? Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobowamu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa