Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 15:2 - Buku Lopatulika

2 Anakhala mfumu zaka zitatu mu Yerusalemu, ndipo dzina la amake linali Maaka mwana wa Abisalomu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Anakhala mfumu zaka zitatu m'Yerusalemu, ndipo dzina la amake linali Maaka mwana wa Abisalomu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Adakhala mfumu mu Yerusalemu zaka zitatu. Mai wake anali Maaka, mwana wa Abisalomu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka zitatu. Amayi ake anali Maaka, mwana wa Abisalomu.

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 15:2
6 Mawu Ofanana  

Nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka makumi anai mphambu chimodzi, ndipo dzina la amake linali Maaka mwana wa Abisalomu.


Ndipo anamchotsera Maaka amake ulemu wa make wa mfumu, popeza iye anapanga fanizo lolaula; ndipo Asa analikha fano lake, nalitentha ku mtsinje wa Kidroni.


Yehosafati anali wa zaka makumi atatu mphambu zisanu, pamene analowa ufumu, nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu mu Yerusalemu. Ndi dzina la amake linali Azuba mwana wa Sili.


Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha Yerobowamu, Abiya analowa ufumu wa Yuda.


Anakhala mfumu m'Yerusalemu zaka zitatu; ndi dzina la make ndiye Mikaya mwana wamkazi wa Uriyele wa ku Gibea. Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobowamu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa