Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 15:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha mfumu Yerobowamu mwana wa Nebati, Abiya analowa ufumu wa Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo chaka chakhumi mphambu zisanu ndi zitatu cha mfumu Yerobowamu mwana wa Nebati, Abiya analowa ufumu wa Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Pa chaka cha 18 cha ufumu wa Yerobowamu mwana wa Nebati, Abiya adaloŵa ufumu wa ku Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wa Yeroboamu mwana wa Nebati, Abiya anakhala mfumu ya Yuda,

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 15:1
4 Mawu Ofanana  

Nagona Rehobowamu ndi makolo ake, naikidwa kwa makolo ake m'mzinda wa Davide. Ndipo dzina la amake linali Naama Mwamoni, nalowa ufumu m'malo mwake Abiya mwana wake.


wakhumi ndi chisanu ndi chiwiri Heziri, wakhumi ndi chisanu ndi chitatu Hapizeze,


Ndi pambuyo pake anatenga Maaka mwana wamkazi wa Abisalomu; ndipo anambalira Abiya, ndi Atai, ndi Ziza, ndi Selomiti.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa