1 Mafumu 13:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo onani, anthu anapitapo naona mtembo wogwera m'njiramo, ndi mkango uli chiimire pafupi ndi mtembo, nadzanena m'mzinda m'mene munakhala mneneri wokalamba uja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo onani, anthu anapitapo naona mtembo wogwera m'njiramo, ndi mkango uli chiimire pafupi ndi mtembo, nadzanena m'mudzi m'mene munakhala mneneri wokalamba uja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Anthu ena amene ankapita mumseumo, adaona mtembo uli gone, mkango utaima pambali pake. Ndipo adapita namakasimbira anzao mu mzinda za zimene adaaona pamseu paja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo taonani, anthu ena amene ankapita mu msewumo anaona mtembowo uli pansi potero, mkango utayima pa mbali pa mtembo uja ndipo anapita nakafotokozera anthu mu mzinda umene mumakhala mneneri wokalamba uja. Onani mutuwo |