1 Mafumu 13:13 - Buku Lopatulika13 Nanena ndi ana ake, Ndimangireni mbereko pabulu. Namangira iwo mbereko pabulu, naberekekapo iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Nanena ndi ana ake, Ndimangireni mbereko pa bulu. Namangira iwo mbereko pa bulu, naberekekapo iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Bambo uja adauza ana akewo kuti, “Mangireni chishalo pa bulu.” Anawo adamanga chishalocho pa bulu, ndipo nkhalamba ija idakwerapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo abambo aja anati kwa ana akewo, “Mangireni chishalo pa bulu.” Anawo atamangirira chishalo pa bulu, nkhalambayo inakwera buluyo Onani mutuwo |