1 Mafumu 13:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo atate wao anati kwa iwo, Wapitira njira yiti? Popeza ana ake adaona njira analowera munthu wa Mulungu anachokera ku Yudayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo atate wao anati kwa iwo, Wapitira njira yiti? Popeza ana ake adaona njira analowera munthu wa Mulungu anachokera ku Yudayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndipo bambo wao uja adaŵafunsa kuti, “Kodi adadzera njira iti?” Ana akewo adamlangiza njira imene adadzera mneneri wa Mulungu wochokera ku Yuda uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Abambo awo aja anawafunsa kuti, “Kodi wadzera njira iti?” Ana akewo anamufotokozera njira imene munthu wa Mulungu wochokera ku Yudayo anadzera. Onani mutuwo |