1 Mafumu 13:10 - Buku Lopatulika10 Tsono iye anayenda njira ina osabwerera njira yomweyo anaidzera pakudza ku Betele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Tsono iye anayenda njira ina osabwerera njira yomweyo anaidzera pakudza ku Betele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Motero mneneriyo adadzera njira ina, osatsata njira imene adaadzera popita ku Betele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho munthu wa Mulunguyo anadzera njira ina ndipo sanatsate njira imene anayendamo pobwera ku Beteliko. Onani mutuwo |