Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mafumu 12:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo anatuma kukamuitana. Ndipo Yerobowamu ndi msonkhano wonse wa Israele anadza, nalankhulana ndi Rehobowamu, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo anatuma kukamuitana. Ndipo Yerobowamu ndi msonkhano wonse wa Israele anadza, nalankhulana ndi Rehobowamu, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Anthu adakamuitana. Choncho Yerobowamu pamodzi ndi anthu onse a ku Israele adadza kwa Rehobowamu namuuza kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Tsono anthu anayitanitsa Yeroboamu, ndipo iye pamodzi ndi gulu lonse la ku Israeli anapita kwa Rehobowamu ndipo anamuwuza kuti,

Onani mutuwo Koperani




1 Mafumu 12:3
4 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali kuti Yerobowamu mwana wa Nebati anachimva akali mu Ejipito, kumene anathawira kuchokera ku maso a Solomoni mfumu, pakuti Yerobowamu anakhala ku Ejipito.


Atate wanu analemeretsa goli lathu, ndipo inu tsono pepuzaniko ntchito zosautsa za atate wanu, ndi goli lolemera lake limene anatisenza, ndipo tidzakutumikirani.


Ndipo anatuma munthu kukamuitana, nadza Yerobowamu ndi Aisraele onse, nalankhula ndi Rehobowamu, ndi kuti,


Koma Abimeleki mwana wa Yerubaala anamuka ku Sekemu kwa abale a amai wake, nanena nao, ndi kwa banja lonse la nyumba ya atate wa amai wake, ndi kuti,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa