1 Mafumu 11:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo machitidwe otsiriza a Solomoni, ndi ntchito zake zonse anazichita, ndi nzeru zake, sizinalembedwe kodi m'buku la machitidwe a Solomoni? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo machitidwe otsiriza a Solomoni, ndi ntchito zake zonse anazichita, ndi nzeru zake, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a Solomoni? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Tsono ntchito zina za Solomoni, ndi zonse zimene adachita, ndiponso nzeru zake, zidalembedwa m'buku la Ntchito za Solomoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Ntchito zina za Solomoni, zonse zomwe anachita komanso za nzeru zake, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya Solomoni? Onani mutuwo |