1 Mafumu 11:10 - Buku Lopatulika10 namlamulira za chinthu chomwechi, kuti asatsate milungu ina, koma iye sanasunge chimene Yehova anachilamula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 namlamulira za chinthu chomwechi, kuti asatsate milungu ina, koma iye sanasunge chimene Yehova anachilamula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 namulamula kuti asatsate milungu ina. Koma Solomoni sadamvere zimene Chauta adamlamulazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngakhale kuti Yehova anamuletsa Solomoni kutsatira milungu ina, iyeyo sanamvere lamulo la Yehova. Onani mutuwo |