1 Mafumu 1:8 - Buku Lopatulika8 Koma Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wake wa Yehoyada, ndi Natani mneneri, ndi Simei, ndi Rei, ndi anthu amphamvu aja adaali ndi Davide, sanali ndi Adoniya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wake wa Yehoyada, ndi Natani mneneri, ndi Simei, ndi Rei, ndi anthu amphamvu aja adali ndi Davide, sanali ndi Adoniya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wa Yehoyada, ndiponso mneneri Natani, Simei, Rei, pamodzi ndi anthu amphamvu aja a Davide, sadamtsate Adoniyayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Koma Zadoki wansembe, Benaya mwana wa Yehoyada, mneneri Natani, Simei ndi Rei ndiponso asilikali amphamvu a Davide sanamutsate Adoniya uja. Onani mutuwo |