1 Mafumu 1:53 - Buku Lopatulika53 Tsono mfumu Solomoni anatuma anthu nakamtsitsa ku guwa la nsembe. Iye nadza, nagwadira mfumu Solomoni; Solomoni nati kwa iye, Pita kwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Tsono mfumu Solomoni anatuma anthu nakamtsitsa ku guwa la nsembe. Iye nadza, nagwadira mfumu Solomoni; Solomoni nati kwa iye, Pita kwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Kenaka mfumu Solomoni adatuma anthu kukamtenga Adoniya kuguwa kuja. Iye adabwera kudzalambira mfumu Solomoni. Ndipo Solomoni adamuuza kuti, “Chabwino, ungathe kupita kunyumba kwako.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Pamenepo Mfumu Solomoni inatuma anthu ndipo anakamutenga paguwa paja. Adoniya anabwera ndi kudzalambira Mfumu Solomoni, ndipo Solomoni anati, “Pita ku nyumba yako.” Onani mutuwo |