1 Mafumu 1:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo Yonatani anayankha, nati kwa Adoniya, Zedi Davide mbuye wathu mfumu walonga Solomoni ufumu: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo Yonatani anayankha, nati kwa Adoniya, Zedi Davide mbuye wathu mfumu walonga Solomoni ufumu: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Tsono Yonatani adayankha kuti, “Iyai, zinthu zaipa uku! Mbuyathu mfumu Davide walonga Solomoni ufumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Yonatani anayankha Adoniya kuti, “Ayi ndithu, zinthu sizili bwino! Mbuye wathu Mfumu Davide walonga Solomoni ufumu. Onani mutuwo |