1 Mafumu 1:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo namwaliyo anali wokongola ndithu, namasunga mfumu namtumikira; koma mfumu sinamdziwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo namwaliyo anali wokongola ndithu, namasunga mfumu namtumikira; koma mfumu sinamdziwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Namwaliyo anali wokongola kwambiri. Tsono adakhala wosamala mfumu ndi kumaitumikira. Koma mfumuyo sidakhale naye malo amodzi namwaliyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mtsikanayo anali wokongola kwambiri ndipo ankasamalira mfumu ndi kumayitumikira, koma mfumuyo sinakhale naye malo amodzi. Onani mutuwo |