1 Mafumu 1:3 - Buku Lopatulika3 Tsono anafunafuna m'malire monse a Israele namwali wokongola, napeza Abisagi wa ku Sunamu, nabwera naye kwa mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Tsono anafunafuna m'malire monse a Israele namwali wokongola, napeza Abisagi wa ku Sunamu, nabwera naye kwa mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Choncho adafunafuna namwali wokongola m'dziko lonse la Israele, ndipo adapeza Abisagi wa ku Sunamu, nabwera naye kwa mfumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kotero anafunafuna mʼdziko lonse la Israeli mtsikana wokongola ndipo anapeza Abisagi wa ku Sunemu, nabwera naye kwa mfumu. Onani mutuwo |