1 Mafumu 1:27 - Buku Lopatulika27 Chinthu ichi chachitika ndi mbuye wanga mfumu kodi, ndipo simunadziwitse mnyamata wanu amene adzakhala pa mpando wachifumu wa mbuye wanga mfumu atamuka iye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Chinthu ichi chachitika ndi mbuye wanga mfumu kodi, ndipo simunadziwitsa mnyamata wanu amene adzakhala pa mpando wachifumu wa mbuye wanga mfumu atamuka iye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Kodi zimenezi mwalamula ndinu mbuyanga mfumu? Bwanji nanga simudauze anthu anu za mwana amene adzakhale pa mpando wanu waufumu m'malo mwanu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Kodi zimenezi mbuye wanga mfumu mwazichita ndinu, osawawuza atumiki anu kuti adziwe amene adzakhale pa mpando waufumu mʼmalo mwanu?” Onani mutuwo |