1 Akorinto 9:19 - Buku Lopatulika19 Pakuti pokhala ndinali mfulu kwa onse, ndinadzilowetsa ndekha ukapolo kwa onse, kuti ndipindule ochuluka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Pakuti pokhala ndinali mfulu kwa onse, ndinadzilowetsa ndekha ukapolo kwa onse, kuti ndipindule ochuluka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ndine mfulu, osati kapolo wa munthu wina aliyense ai, komabe ndidadzisandutsa kapolo wa anthu onse, kuti ndikope anthu ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ngakhale ndine mfulu ndipo sindine kapolo wa munthu, ndimadzisandutsa kapolo wa aliyense kuti ndikope ambiri mmene ndingathere. Onani mutuwo |