1 Akorinto 7:38 - Buku Lopatulika38 Chotero iye amene akwatitsa mwana wake wamkazi achita bwino, ndipo iye wosamkwatitsa achita koposa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Chotero iye amene akwatitsa mwana wake wamkazi achita bwino, ndipo iye wosamkwatitsa achita koposa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Ndiye kuti, munthu wokwatira namwali amene adamtomera, akuchita bwino, koma woleka osamkwatira, akuchita bwino koposa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Choncho amene akukwatira namwali amene ali naye pa ubwenzi, akuchita bwino, koma amene sangakwatire namwaliyo akuchita bwino koposa. Onani mutuwo |