1 Akorinto 6:18 - Buku Lopatulika18 Thawani dama. Tchimo lililonse munthu akalichita lili kunja kwa thupi; koma wachiwerewere achimwira thupi lake la iye yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Thawani dama. Tchimo lililonse munthu akalichita lili kunja kwa thupi; koma wachiwerewere achimwira thupi lake la iye yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Thaŵani dama. Tchimo lina lililonse limene munthu amachita, siliipitsa thupi lake, koma munthu wadama amachimwira thupi lake lomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Thawani dama. Machimo onse amene munthu amachita amakhala kunja kwa thupi lake, koma amene amachita machimo okhudza chigololo, amachimwira thupi lake lomwe. Onani mutuwo |