1 Akorinto 15:53 - Buku Lopatulika53 Pakuti chovunda ichi chiyenera kuvala chisavundi, ndi chaimfa ichi kuvala chosafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Pakuti chovunda ichi chiyenera kuvala chisavundi, ndi chaimfa ichi kuvala chosafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Pakuti thupi lotha kuwolali liyenera kusanduka losatha kuwola, ndipo thupi lotha kufali liyenera kusanduka losatha kufa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Pakuti chovunda chiyenera kuvala chosavunda, ndi thupi ili lakufa liyenera kuvala losafa. Onani mutuwo |