1 Akorinto 15:48 - Buku Lopatulika48 Monga wanthakayo, ateronso anthaka; ndi monga wakumwamba, ateronso akumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Monga wanthakayo, ateronso anthaka; ndi monga wakumwamba, ateronso akumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Anthu onse apansipano ali ngati Adamu wopangidwa ndi dothi uja. Ndipo onse amene ali a Kumwamba, ali ngati Khristu wa Kumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Monga analili munthu wa dziko lapansi, momwemonso anthu onse amene ndi a dziko lapansi. Ndipo monga alili munthu wakumwamba, momwemonso anthu onse amene ndi akumwamba. Onani mutuwo |