1 Akorinto 15:42 - Buku Lopatulika42 Chomwechonso kudzakhala kuuka kwa akufa. Lifesedwa m'chivundi, liukitsidwa m'chisavundi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Chomwechonso kudzakhala kuuka kwa akufa. Lifesedwa m'chivundi, liukitsidwa m'chisavundi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Zidzateronso pamene akufa adzauka. Thupi loikidwa m'nthaka ngati mbeu yofesa, limaola, koma likadzauka, lidzakhala losaola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Zidzaterenso pamene akufa adzauka. Thupi loyikidwa mʼnthaka ngati mbewu limavunda, koma likadzauka lidzakhala losavunda. Onani mutuwo |