Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 15:39 - Buku Lopatulika

39 Nyama yonse siili imodzimodzi; koma ina ndi ya anthu, ndi ina ndiyo nyama ya zoweta, ndi ina ndiyo nyama ya mbalame, ndi ina ya nsomba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

39 Nyama yonse siili imodzimodzi; koma ina ndi ya anthu, ndi ina ndiyo nyama ya zoweta, ndi ina ndiyo nyama ya mbalame, ndi ina ya nsomba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

39 Mnofu sukhala wa mtundu umodzi. Pali mnofu wina wa anthu, wina wa nyama, wina wa mbalame, ndi wina wa nsomba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

39 Mnofu siwofanana. Anthu ali ndi mnofu wa mtundu wina, nyama zili ndi wina, mbalame zili ndi wina, nsomba zili ndi winanso.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 15:39
3 Mawu Ofanana  

koma Mulungu aipatsa thupi monga afuna; ndi kwa mbeu yonse thupi lakelake.


Palinso matupi am'mwamba, ndi matupi apadziko: koma ulemerero wa lam'mwamba ndi wina, ndi ulemerero wa lapadziko ndi winanso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa