1 Akorinto 15:36 - Buku Lopatulika36 Wopusa iwe, chimene uchifesa wekha sichikhalitsidwanso chamoyo, ngati sichifa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Wopusa iwe, chimene uchifesa wekha sichikhalitsidwanso chamoyo, ngati sichifa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Ati kupusa ati! Mbeu imene umafesa, siingamere ndi kukhala moyo itapanda kufa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Wopusa iwe! Chimene mudzala sichikhala ndi moyo pokhapokha chitayamba chafa. Onani mutuwo |