1 Akorinto 15:30 - Buku Lopatulika30 Nanga ifenso tili m'moopsa bwanji nthawi zonse? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Nanga ifenso tili m'moopsa bwanji nthawi zonse? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Nanga pamenepo ifenso timakhaliranji m'zoopsa nthaŵi zonse? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndipo kwa ife, tikuyikiranji moyo wathu pachiswe nthawi ndi nthawi? Onani mutuwo |