1 Akorinto 15:21 - Buku Lopatulika21 Pakuti monga imfa inadza mwa munthu, kuuka kwa akufa kunadzanso mwa munthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pakuti monga imfa inadza mwa munthu, kuuka kwa akufa kunadzanso mwa munthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pakuti monga imfa idadza pansi pano kudzera mwa munthu wina, momwemonso kuuka kwa akufa kudadza kudzera mwa munthu wina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti monga imfa inadza kudzera mwa munthu, kuuka kwa akufa kwabweranso kudzera mwa munthu. Onani mutuwo |