1 Akorinto 15:20 - Buku Lopatulika20 Koma tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa, chipatso choyamba cha iwo akugona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa, chipatso choundukula cha iwo akugona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma ai, Khristu adauka ndithu kwa akufa. Pakati pa onse amene adafa, ndiye woyamba kuuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma nʼzoonadi kuti Khristu anaukitsidwa kwa kufa, chipatso choyamba cha onse ogona tulo. Onani mutuwo |