1 Akorinto 15:14 - Buku Lopatulika14 ndipo ngati Khristu sanaukitsidwe kulalikira kwathu kuli chabe, chikhulupiriro chanunso chili chabe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndipo ngati Khristu sanaukitsidwa kulalikira kwathu kuli chabe, chikhulupiriro chanunso chili chabe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono ngati Khristu sadauke, kulalika kwathu nkwachabe, ndipo chikhulupiriro chanu nchachabenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ndipo ngati Khristu sanaukitsidwe, ndiye kuti kulalikira kwathu nʼkopanda ntchito, ndipo chikhulupiriro chanu nʼchopandanso ntchito. Onani mutuwo |